Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 19:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Tsiku limenelo Israyeli ndi Aigupto ndi Asuri atatuwa, adzakhala mdalitso pakati pa dziko lapansi;

25. pakuti Yehova wa makamu wadalitsa iwo, ndi kuti, Odalitsika Aigupto anthu anga, ndi Asuri nchito ya manja anga, ndi Israyeli colowa canga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 19