Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 19:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku limenelo padzakhala khwalala locokera m'Aigupto kunka ku Asuri, ndipo M-asuri adzafika ku Aigupto, ndi M-aigupto adzafika ku Asuri, ndipo Aaigupto adzapembedzera pamodzi ndi Aasuri.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 19

Onani Yesaya 19:23 nkhani