Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 18:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi imeneyo mphatso idzaperekedwa kwa Yehova wa makamu, mtundu wa anthu atari ndi osalala, yocokera kwa mtundu woopsya cikhalire cao; mtundu umene uyesa dziko ndi kupondereza pansi, umene dziko lace nyanja ziligawa, ku malo a dzina la Yehova wa makamu, phiri la Ziyoni.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 18

Onani Yesaya 18:7 nkhani