Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 18:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

limene litumiza mithenga panyanja m'ngalawa zatnabungwa zoyenda m'madzi, ndi kuti, Mukani, inu mithenga yoyenda msanga msanga ku mtundu wa anthu atari ndi osalala, kwa mtundu woopsya cikhalire cao, mtundu umene uyesa dziko ndi kupondereza pansi, umene dziko lace nyanja ziligawa!

Werengani mutu wathunthu Yesaya 18

Onani Yesaya 18:2 nkhani