Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 14:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usakondwere, lwe Filistia, wonsewe, potyoka ndodo inakumenya; pakuti m'muzu wa njoka mudzaturuka mphiri, ndimo cipatso cace cidzakhala njoka yamoto youluka.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 14

Onani Yesaya 14:29 nkhani