Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 12:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Tsiku lomwelo mudzati, Muyamikire Yehova, bukitsani dzina lace, mulalikire macitidwe ace mwa mitundu ya anthu, munene kuti dzina lace lakwezedwa.

5. Muyimbire Yehova; pakuti wacita zaulemerero; cidziwike ici m'dziko lonse.

6. Tapfuula, takuwa iwe, wokhala m'Ziyoni, cifukwa Woyera wa Israyeli wa m'kati mwako ali wamkuru.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 12