Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma ndi cilungamo adzaweruza aumphawi, nadzadzudzulira ofatsa a m'dziko moongoka; ndipo adzamenya dziko lapansi ndi cibonga ca kukamwa kwace, nadzapha oipa ndi mpweya wa milomo yace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 11

Onani Yesaya 11:4 nkhani