Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 11:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye adzaimika mbendera ya amitundu, ndipo adzasonkhanitsa oingitsidwa a Israyeli, namema obalalika a Yuda, kucokera ku madera anai a dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 11

Onani Yesaya 11:12 nkhani