Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 11:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, kuti Ambuye adzabweza kaciwiri ndi dzanja lace anthu ace otsala ocokera ku Asuri, ndi ku Aigupto, ndi ku Patirosi, ndi ku Kusi, ndi ku Elamu, ndi ku Sinara, ndi ku Hamati, ndi ku zisumbu za m'nyanja yamcere.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 11

Onani Yesaya 11:11 nkhani