Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 10:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, kuti katundu wace adzacoka pa phewa lako, ndi gori lace pakhosi pako; ndipo gori lidzathedwa cifukwa ca kudzoza mafuta.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10

Onani Yesaya 10:27 nkhani