Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene mutambasula manja anu, ndidzakubisirani inu maso anga; inde pocurukitsa mapemphero anu Ine sindidzamva; manja anu adzala mwazi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:15 nkhani