Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 9:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma wakudzitamandira adzitamandire adzikweze umo, kuti ali wakuzindikira, ndi kundidziwa Ine, kuti ndine Yehova wakucita zokoma mtima, ciweruziro, ndi cilungamo m'dziko lapansi, pakuti m'menemo ndikondwerera, ati. Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 9

Onani Yeremiya 9:24 nkhani