Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 9:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, wanzeru asadzitamandire m'nzeru zace, wamphamvu asadzitamandire m'mphamvu yace, wacuma asadzitamandire m'cuma cace;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 9

Onani Yeremiya 9:23 nkhani