Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo otsala onse amene akutsala pa banja loipa ili adzasankha imfa koposa moyo, ndiwo amene atsala m'malo monse m'mene ndinawaingiramo, ati Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 8

Onani Yeremiya 8:3 nkhani