Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 8:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, mau a kulira kwa mwana wamkazi wa anthu anga ocokera ku dziko lakutari: Kodi m'Ziyoni mulibe Yehova? Kodi mulibe Mfumu yace? Cifukwa canji andiputa Ine ndi mafano ao osema, ndi zacabe zacilendo?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 8

Onani Yeremiya 8:19 nkhani