Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 8:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tikhaliranji ife? tasonkhanani, tilowe m'midzi yamalinga, tikhale cete m'menemo; pakuti Yehova Mulungu wathu watikhalitsa ife cete, natipatsa ife madzi a ndulu timwe, pakuti tamcimwira Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 8

Onani Yeremiya 8:14 nkhani