Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 6:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ananu a Benjamini, pulumukani pothawa pakati pa Yerusalemu, ombani lipenga m'Tekoa, kwezani cizindikiro m'Beti-hakeremu; pakuti caoneka coipa coturuka m'mpoto ndi kuononga kwakukulu.

2. Ndidzacotsa mwana wamkazi wa Ziyoni mkazi wokoma ndi wololopoka.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 6