Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ananu a Benjamini, pulumukani pothawa pakati pa Yerusalemu, ombani lipenga m'Tekoa, kwezani cizindikiro m'Beti-hakeremu; pakuti caoneka coipa coturuka m'mpoto ndi kuononga kwakukulu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 6

Onani Yeremiya 6:1 nkhani