Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 52:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali caka ca makumi atatu ndi zisanu ndi ziwiri ca undende wa Yehoyakimu mfumu ya Yuda, mwezi wakhumi ndi iwiri, tsiku la makumi awiri ndi asanu la mwezi, Evili-Merodaki mfumu ya ku Babulo anaweramutsa mutu wa Yehoyakimu mfumu ya Yuda, namturutsa iye m'ndende;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 52

Onani Yeremiya 52:31 nkhani