Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 52:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi zikho, ndi zopalira moto, ndi mbale, ndi miphika, ndi zoikapo nyali, ndi zipande, ndi mitsuko; ndi golidi, wa zija zagolidi, ndi siliva, wa zija zasiliva, kapitao wa alonda anazicotsa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 52

Onani Yeremiya 52:19 nkhani