Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 51:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nolani mibvi; gwirani zolimba zikopa; Yehova waukitsa mtima wa mafumu a Amedi; cifukwa alingalirira Babulo kuti amuononge; pakuti ndi kubwezera cilango kwa Yehova; kubwezera cilango cifukwa ca Kacisi wace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:11 nkhani