Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 50:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mtundu wa anthu udzaturuka kumpoto kudzamenyana naye, udzacititsa dziko lace bwinja, losakhalamo anthu; athawa, apita, anthu ndi nyama.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:3 nkhani