Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 5:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala: pamene mudzati, Cifukwa canji Yehova Mulungu wathu aticitira ife zonse izi? ndipo udzayankha kwa iwo, Monga ngati mwandisiya Ine, ndi kutumikira milungu yacilendo m'dziko lanu, momwemo mudzatumikira alendo m'dziko siliri lanu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5

Onani Yeremiya 5:19 nkhani