Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 5:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndidzatengera pa inu mtundu wa anthu akutari, inu nyumba ya Israyeli, ati Yehova; ndi mtundu wolimba, ndi mtundu wakalekale, mtundu umene cinenero cace simudziwa, ngakhale kumva zonena zao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5

Onani Yeremiya 5:15 nkhani