Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 5:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yehova Mulungu wa makamu atero, Cifukwa munena mau awa, taona, ndidzayesa mau anga akhale m'kamwa mwako ngati moto, anthu awa ndidzayesa nkhuni, ndipo udzawatha iwo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5

Onani Yeremiya 5:14 nkhani