Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona ndidzakutengera mantha, ati Ambuye, Yehova wa makamu, akucokera kwa onse amene akuzungulira iwe; ndipo mudzaingitsidwa yense kulozera maso ace, ndipo palibe amene adzasonkhanitsa osocera.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:5 nkhani