Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzacititsa Elamu mantha pamaso pa amaliwongo ao, ndi pamaso pa iwo ofuna moyo wao; ndipo ndidzatengera coipa pa iwo, mkwiyo wanga waukali, ati Yehova; ndipo ndidzatumiza lupanga liwalondole, mpaka nditawatha;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:37 nkhani