Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pa Elamu ndidzatengera mphepo zinai ku mbali zinai za mlengalenga, ndidzamwaza iwo ku mphepo zonsezo; ndipo sikudzakhala mtundu kumene opitikitsidwa a Elamu sadzafikako.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:36 nkhani