Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mahema ao ndi zoweta zao adzazilanda, adzadzitengera nsaru zocingira zao, ndi katundu wao yense, ndi ngamila zao; ndipo adzapfuulira iwo, Mantha ponse ponse.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:29 nkhani