Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tamvani uphungu wa Yehova, umene waupangira pa Edomu; ndi zimene walingalirira okhala m'Temani, ndithu adzawakoka, ana ang'ono a zoweta; ndithu adzayesa busa lao bwinja pamodzi nao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:20 nkhani