Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, wina adzakwerera mudzi wolimba ngati mkango wocokera ku Yordano wosefuka; koma dzidzidzi ndidzamthamangitsa amcokere; ndipo ali yense amene asankhidwa, ndidzamuika woyang'anira wace, pakuti wakunga Ine ndani? adzandiikira nthawi ndani? ndipo mbusa adzaima pamaso panga ndani?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:19 nkhani