Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 48:46-47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

46. Tsoka iwe, Moabu! anthu a Kemosi athedwa; pakuti ana ako amuna atengedwa ndende, ndi ana ako akazi atengedwa ndende.

47. Koma ndidzabwezanso undende wa Moabu masiku akumariza, ati Yehova. Ziweruzo za Moabu ndi zomwezi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48