Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 48:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo amene anathawa aima opanda mphamvu pansi pa mthunzi wa Hesiboni; pakuti moto waturuka m'Hesiboni, ndi malawi a moto m'kati mwa Sihoni, nadya ngondya ya Moabu, ndi pakati pamtu pa ana a phokoso,

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48

Onani Yeremiya 48:45 nkhani