Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 48:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuyambira kupfuula kwa Hesiboni mpaka ku Eleale, mpaka ku Yahazi anakweza mau, kuyambira pa Zoari mpaka ku Horonaimu, ku Egilati-Selisiya; pakuti pa madzi a ku Nimurimu komwe padzakhala mabwinja.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48

Onani Yeremiya 48:34 nkhani