Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 48:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palibenso kutamanda Moabu; m'Hesiboni anamlingiririra zoipa, ndi kuti, Tiyeni, tiwathe asakhalenso mtundu waanthu. Iwenso, Madimeni, udzatontholetsedwa, lupanga lidzakulondola iwe.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48

Onani Yeremiya 48:2 nkhani