Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 45:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi udzifunira wekha zinthu zazikuru? usazifune; pakuti, taona, ndidzatengera zoipa pa anthu onse, ati Yehova: koma moyo wako ndidzakupatsa iwe ngati cofunkha m'malo monse m'mene mupitamo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 45

Onani Yeremiya 45:5 nkhani