Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 44:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi mwaiwala zoipa za makolo anu, ndi zoipa za mafumu a Yuda, ndi zoipa za akazi ao, ndi zoipa zanu, ndi za akazi anu, zimene anazicita m'dziko la Yuda, ndi m'miseu ya Yerusalemu?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 44

Onani Yeremiya 44:9 nkhani