Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 44:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova atero: Taonani, ndidzapereka Farao Hofra mfumu ya Aigupto m'manja a adani ace, ndi m'manja a iwo akufuna moyo wace; monga ndinapereka Zedekiya mfumu ya Yuda m'manja a Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo mdani wace, amene anafuna moyo wace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 44

Onani Yeremiya 44:30 nkhani