Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 43:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo ananena Azariya mwana wace wa Hosaya, ndi Yohanani mwana wace wa Kareya, ndi anthu onse odzikuza, nati kwa Yeremiya, Unena zonama; Yehova Mulungu wathu sanakutumiza iwe kudzanena, Musalowe m'Aigupto kukhala m'menemo;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 43

Onani Yeremiya 43:2 nkhani