Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 42:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo lero ndakufotokozerani, ndipo simunamva mau a Yehova Mulungu wanu m'cinthu ciri conse cimene Iye wanditumira ine naco kwa inu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 42

Onani Yeremiya 42:21 nkhani