Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 42:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mwanyenga m'miyoyo yanu; pakuti mwandituma ine kwa Yehova Mulungu wanu, ndi kuti, Mutipempherere ife kwa Yehova Mulungu wathu; ndipo monga mwa zonse Yehova Mulungu wathu adzanena, momwemo mutifotokozere ife; ndipo tidzacita.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 42

Onani Yeremiya 42:20 nkhani