Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 42:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Monga mkwiyo wanga ndi ukali wanga wathiridwa kwa okhala m'Yerusalemu, momwemo ukali wanga udzathiridwa pa inu, pamene mudzalowa m'Aigupto; ndipo mudzakhala citukwano, ndi cizizwitso, ndi citemberero, ndi citonzo; ndipo simudzaonanso malo ano.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 42

Onani Yeremiya 42:18 nkhani