Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 42:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kudzatero ndi anthu onse akulozetsa nkhope zao anke ku Aigupto kuti akhale kumeneko; adzafa ndi lupanga, ndi njala, ndi caola; ndipo wa iwo sadzatsala kapena kupulumuka ku coipa cimene ndidzatengera pa iwo ngakhale mmodzi yense.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 42

Onani Yeremiya 42:17 nkhani