Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 41:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yohanani mwana wace wa Kareya ndi akazembe onse a makamu amene anali naye, anatenga anthu onse otsala a ku Mizipa, amene anawabweza kwa Ismayeli mwana wace wa Netaniya atapha Gedaliya mwana wace wa Ahikamu, anthu a nkhondo, ndi akazi, ndi ana, ndi adindo, amene anawabwezanso ku Gibeoni;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 41

Onani Yeremiya 41:16 nkhani