Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 40:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo anadza kwa Gedaliya ku Mizipa, Ismayeli mwana wa Netaniya, ndi Yohanani ndi Yonatani ana a Kareya, ndi Saraya mwana wa Tanumeti, ndi ana a Efai wa ku Netofa, ndi Jezaniya mwana wa munthu wa ku Maaka, iwo ndi anthu ao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 40

Onani Yeremiya 40:8 nkhani