Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 40:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene akuru onse a makamu amene anali m'minda, iwo ndi anthu ao, anamva kuti mfumu ya ku Babulo adamuika Gedaliya mwana wa Ahikamu wolamulira dziko, nampatsira amuna, ndi akazi, ndi ana, ndi aumphawi a m'dzikomo, a iwo amene sanatengedwa ndende kunka nao ku Babulo;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 40

Onani Yeremiya 40:7 nkhani