Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 40:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono asanabwerere iye anati, Bweratu kwa Gedaliya mwana wa Ahikamu, mwana wa Safani, amene mfumu ya ku Babulo inamyesa wolamulira midzi ya Yuda, nukhale naye pakati pa anthu; kapena pita kuli konse ukuyesa koyenera kupitako. Ndipo kapitao wa alonda anampatsa iye phoso ndi mtulo, namleka amuke.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 40

Onani Yeremiya 40:5 nkhani