Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 40:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, taona, ndikumasula iwe lero maunyolo ali pa manja ako. Kukakukomera kudza nane ku Babulo, idza, ndipo ndidzakusamalira bwino; koma kukakuipira kudza nane ku Babulo, tsala; taona, dziko lonse liri pamaso pako; kuli konse ukuyesa kwabwino kapena koyenera kupitako, pita kumeneko.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 40

Onani Yeremiya 40:4 nkhani