Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 40:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco pamene Ayuda onse okhala m'Moabu ndi mwa ana a Amoni, ndi m'Edomu, ndi amene anali m'maiko monse, anamva kuti mfumu ya ku Babulo inasiya otsala a Yuda, ndi kuti inamuika Gedaliya mwana wa Ahikamu, mwana wa Safani wolamulira wao;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 40

Onani Yeremiya 40:11 nkhani