Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 4:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Matumbo anga, matumbo anga! ndipoteka pamtima panga peni peni; mtima wanga sukhala pansi m'kati mwanga; sindithai kutonthola; pakuti wamva, moyo wanga, mau a lipenga, mbiri ya nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:19 nkhani